Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 32 - صٓ - Page - Juz 23
﴿فَقَالَ إِنِّيٓ أَحۡبَبۡتُ حُبَّ ٱلۡخَيۡرِ عَن ذِكۡرِ رَبِّي حَتَّىٰ تَوَارَتۡ بِٱلۡحِجَابِ ﴾
[صٓ: 32]
﴿فقال إني أحببت حب الخير عن ذكر ربي حتى توارت بالحجاب﴾ [صٓ: 32]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adati: “Ndikukonda zinthu zabwino chifukwa chokumbukira Mbuye wanga,” kufikira pomwe (akavalowo) adabisika kuseri kwa chotsekereza (poikidwa m’makola mwawo pomwe iye amafunitsitsa kumawaonabe) |