×

Ndipo iwo ali kudabwa kuti Mtumwi wadza kwa iwo kuchokera pakati pawo. 38:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:4) ayat 4 in Chichewa

38:4 Surah sad ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 4 - صٓ - Page - Juz 23

﴿وَعَجِبُوٓاْ أَن جَآءَهُم مُّنذِرٞ مِّنۡهُمۡۖ وَقَالَ ٱلۡكَٰفِرُونَ هَٰذَا سَٰحِرٞ كَذَّابٌ ﴾
[صٓ: 4]

Ndipo iwo ali kudabwa kuti Mtumwi wadza kwa iwo kuchokera pakati pawo. Ndipo anthu osakhulupirira amati, “Uyu ndi munthu wamatsenga ndiponso wabodza!”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وعجبوا أن جاءهم منذر منهم وقال الكافرون هذا ساحر كذاب, باللغة نيانجا

﴿وعجبوا أن جاءهم منذر منهم وقال الكافرون هذا ساحر كذاب﴾ [صٓ: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo anadabwa atawadzera mchenjezi wochokera mwa iwo. Ndipo osakhulupirira adati: “Uyu ndiwamatsenga; ngwabodza lamkunkhuniza!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek