×

Ndi Atumwi amene Ife takuuza kale mbiri yawo ndi Atumwi amene sitidakuuze 4:164 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:164) ayat 164 in Chichewa

4:164 Surah An-Nisa’ ayat 164 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 164 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿وَرُسُلٗا قَدۡ قَصَصۡنَٰهُمۡ عَلَيۡكَ مِن قَبۡلُ وَرُسُلٗا لَّمۡ نَقۡصُصۡهُمۡ عَلَيۡكَۚ وَكَلَّمَ ٱللَّهُ مُوسَىٰ تَكۡلِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 164]

Ndi Atumwi amene Ife takuuza kale mbiri yawo ndi Atumwi amene sitidakuuze ayi, ndipo ndi Mose Mulungu adalankhula naye mwachindunji

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ورسلا قد قصصناهم عليك من قبل ورسلا لم نقصصهم عليك وكلم الله, باللغة نيانجا

﴿ورسلا قد قصصناهم عليك من قبل ورسلا لم نقصصهم عليك وكلم الله﴾ [النِّسَاء: 164]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (tidavumbulutsanso chivumbulutso) kwa atumiki omwe takusimbira kale nkhani zawo komanso kwa atumiki ena omwe sitinakusimbire (nkhani zawo); ndipo Allah adayankhula ndi Mûsa mwachindunji
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek