×

Ife tavumbulutsa kwa iwe monga momwe tidavumbulutsira kwa Nowa ndi kwa Atumwi 4:163 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:163) ayat 163 in Chichewa

4:163 Surah An-Nisa’ ayat 163 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 163 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿۞ إِنَّآ أَوۡحَيۡنَآ إِلَيۡكَ كَمَآ أَوۡحَيۡنَآ إِلَىٰ نُوحٖ وَٱلنَّبِيِّـۧنَ مِنۢ بَعۡدِهِۦۚ وَأَوۡحَيۡنَآ إِلَىٰٓ إِبۡرَٰهِيمَ وَإِسۡمَٰعِيلَ وَإِسۡحَٰقَ وَيَعۡقُوبَ وَٱلۡأَسۡبَاطِ وَعِيسَىٰ وَأَيُّوبَ وَيُونُسَ وَهَٰرُونَ وَسُلَيۡمَٰنَۚ وَءَاتَيۡنَا دَاوُۥدَ زَبُورٗا ﴾
[النِّسَاء: 163]

Ife tavumbulutsa kwa iwe monga momwe tidavumbulutsira kwa Nowa ndi kwa Atumwi ena amene anadza pambuyo pa iye. Ndipo tidavumbulutsa kwa Abrahamu, Ishimayeli, Isake, Yakobo ndi a mitundu, Yesu, Yobu, Yona, Aroni ndi Solomoni ndipo Davide tidamupatsa Buku la Masalimo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنا أوحينا إليك كما أوحينا إلى نوح والنبيين من بعده وأوحينا إلى, باللغة نيانجا

﴿إنا أوحينا إليك كما أوحينا إلى نوح والنبيين من بعده وأوحينا إلى﴾ [النِّسَاء: 163]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, takuvumbulutsira (chivumbulutso) monga momwe tidamuvumbulutsira Nuh (Nowa) ndi aneneri amene anadza pambuyo pake. Ndipo tidamuvumbulutsiranso Ibrahim, Ismail, Ishâq, Ya’qub ndi mbumba yake. Ndipo (tidamuvumbulutsiranso) Isa (Yesu), Ayyub (Yobu), Yunus (Yona), Haarun (Aroni) ndi Sulaiman, ndipo Daud tidampatsa Zabur (Masalimo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek