×

Ndipo ngati inu muopa kuti asiyana, sankhani nkhoswe kuchokera kwa m’bale wa 4:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:35) ayat 35 in Chichewa

4:35 Surah An-Nisa’ ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 35 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَإِنۡ خِفۡتُمۡ شِقَاقَ بَيۡنِهِمَا فَٱبۡعَثُواْ حَكَمٗا مِّنۡ أَهۡلِهِۦ وَحَكَمٗا مِّنۡ أَهۡلِهَآ إِن يُرِيدَآ إِصۡلَٰحٗا يُوَفِّقِ ٱللَّهُ بَيۡنَهُمَآۗ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ عَلِيمًا خَبِيرٗا ﴾
[النِّسَاء: 35]

Ndipo ngati inu muopa kuti asiyana, sankhani nkhoswe kuchokera kwa m’bale wa mwamuna ndiponso nkhoswe kuchokera kwa m’bale wa mkazi ngati iwo akufuna kuyanjanitsidwa, ndipo Mulungu adzawayanjanitsa pakati pawo. Ndithudi Mulungu ndi wodziwa ndi wozindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن خفتم شقاق بينهما فابعثوا حكما من أهله وحكما من أهلها إن, باللغة نيانجا

﴿وإن خفتم شقاق بينهما فابعثوا حكما من أهله وحكما من أهلها إن﴾ [النِّسَاء: 35]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (inu aweruzi) ngati muopa mkangano pakati pawo (pa mwamuna ndi mkazi wake), tumizani nkhoswe ya kuchimuna ndi nkhoswe ya kuchikazi. Ngati iwo atafuna kuyanjanitsa, Allah awapatsa mphamvu zoyanjanitsira pakati pawo (okanganawo). Allah Ngodziwa nkhani zobisika, ndiponso Ngodziwa nkhani zoonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek