×

Iwo amene ndi oumira ndipo amauza anzawo kuti akhalenso oumira, amene amabisa 4:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:37) ayat 37 in Chichewa

4:37 Surah An-Nisa’ ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 37 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿ٱلَّذِينَ يَبۡخَلُونَ وَيَأۡمُرُونَ ٱلنَّاسَ بِٱلۡبُخۡلِ وَيَكۡتُمُونَ مَآ ءَاتَىٰهُمُ ٱللَّهُ مِن فَضۡلِهِۦۗ وَأَعۡتَدۡنَا لِلۡكَٰفِرِينَ عَذَابٗا مُّهِينٗا ﴾
[النِّسَاء: 37]

Iwo amene ndi oumira ndipo amauza anzawo kuti akhalenso oumira, amene amabisa chuma chimene Mulungu adawapatsa mwachifundo chake. Ndipo Ife tawakonzera anthu osakhulupirira chilango chochititsa manyazi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الذين يبخلون ويأمرون الناس بالبخل ويكتمون ما آتاهم الله من فضله وأعتدنا, باللغة نيانجا

﴿الذين يبخلون ويأمرون الناس بالبخل ويكتمون ما آتاهم الله من فضله وأعتدنا﴾ [النِّسَاء: 37]

Khaled Ibrahim Betala
“Omwe amachita umbombo ndi kulamula anthu kuchita umbombo ndi kubisa zabwino zomwe Allah wawapatsa. Komatu osakhulupirira tawakonzera chilango choyalutsa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek