Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 5 - مُحمد - Page - Juz 26
﴿سَيَهۡدِيهِمۡ وَيُصۡلِحُ بَالَهُمۡ ﴾
[مُحمد: 5]
﴿سيهديهم ويصلح بالهم﴾ [مُحمد: 5]
Khaled Ibrahim Betala “Awaongolera (ku zimene zingawapindulitse pa dziko lapansi ndi patsiku lachimaliziro) ndi kuwakonzera zinthu zawo ndi chikhalidwe chawo |