Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 7 - مُحمد - Page - Juz 26
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِن تَنصُرُواْ ٱللَّهَ يَنصُرۡكُمۡ وَيُثَبِّتۡ أَقۡدَامَكُمۡ ﴾
[مُحمد: 7]
﴿ياأيها الذين آمنوا إن تنصروا الله ينصركم ويثبت أقدامكم﴾ [مُحمد: 7]
Khaled Ibrahim Betala “E inu amene mwakhulupirira! Ngati muteteza chipembedzo cha Allah, (Iye) adzakutetezani (kwa adani anu) ndi kulimbikitsa mapazi anu (pa nkhondo) |