×

oh inu anthu otsatira Buku! Tsopano mtumwi wathu wadza kwa inu kudzaulula 5:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:19) ayat 19 in Chichewa

5:19 Surah Al-Ma’idah ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 19 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿يَٰٓأَهۡلَ ٱلۡكِتَٰبِ قَدۡ جَآءَكُمۡ رَسُولُنَا يُبَيِّنُ لَكُمۡ عَلَىٰ فَتۡرَةٖ مِّنَ ٱلرُّسُلِ أَن تَقُولُواْ مَا جَآءَنَا مِنۢ بَشِيرٖ وَلَا نَذِيرٖۖ فَقَدۡ جَآءَكُم بَشِيرٞ وَنَذِيرٞۗ وَٱللَّهُ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[المَائدة: 19]

oh inu anthu otsatira Buku! Tsopano mtumwi wathu wadza kwa inu kudzaulula poyera chifuniro chathu patapita nthawi yaitali imene kudalibe Atumwi, kuti mwina mungadzanene kuti: “Sikudabwere kwa ife wodzatiuza nkhani zabwino kapena kudzatichenjeza.” Ndipo Mulungu ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأهل الكتاب قد جاءكم رسولنا يبين لكم على فترة من الرسل أن, باللغة نيانجا

﴿ياأهل الكتاب قد جاءكم رسولنا يبين لكم على فترة من الرسل أن﴾ [المَائدة: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu anthu a buku! Ndithudi, wakudzerani Mtumiki Wathu yemwe akukufotokozerani inu, pa nthawi yopanda atumiki, kuti musadzanene kuti: “Sadadze kwa ife wonena nkhani zabwino ndiwochenjeza.” Choncho wakudzeranidi wonena nkhani zabwino ndi wochenjeza. Ndipo Allah Ngokhoza chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek