Quran with Chichewa translation - Surah An-Najm ayat 56 - النَّجم - Page - Juz 27
﴿هَٰذَا نَذِيرٞ مِّنَ ٱلنُّذُرِ ٱلۡأُولَىٰٓ ﴾
[النَّجم: 56]
﴿هذا نذير من النذر الأولى﴾ [النَّجم: 56]
Khaled Ibrahim Betala “Uyu (Mtumiki) ndimchenjezi mwa achenjezi oyamba (amene adachenjezedwa nawo anthu a mibadwo yakale) |