Quran with Chichewa translation - Surah An-Najm ayat 60 - النَّجم - Page - Juz 27
﴿وَتَضۡحَكُونَ وَلَا تَبۡكُونَ ﴾
[النَّجم: 60]
﴿وتضحكون ولا تبكون﴾ [النَّجم: 60]
Khaled Ibrahim Betala “Mungoseka (mwachipongwe) ndipo simukulira (pamene mukuimva monga momwe akuchitira okhulupirira) |