Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 24 - المُلك - Page - Juz 29
﴿قُلۡ هُوَ ٱلَّذِي ذَرَأَكُمۡ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَإِلَيۡهِ تُحۡشَرُونَ ﴾
[المُلك: 24]
﴿قل هو الذي ذرأكم في الأرض وإليه تحشرون﴾ [المُلك: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Iye ndi amene adakuchulukitsani pa dziko ndipo kwa Iye (Yekha) ndiko mudzasonkhanitsidwa (kuti adzakuwerengereni ndi kukulipirani) |