Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qalam ayat 8 - القَلَم - Page - Juz 29
﴿فَلَا تُطِعِ ٱلۡمُكَذِّبِينَ ﴾
[القَلَم: 8]
﴿فلا تطع المكذبين﴾ [القَلَم: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho, usawamvere otsutsa; (usasiye zimene uli nazo ngakhale sakugwirizana nazo) |