Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 182 - الأعرَاف - Page - Juz 9
﴿وَٱلَّذِينَ كَذَّبُواْ بِـَٔايَٰتِنَا سَنَسۡتَدۡرِجُهُم مِّنۡ حَيۡثُ لَا يَعۡلَمُونَ ﴾
[الأعرَاف: 182]
﴿والذين كذبوا بآياتنا سنستدرجهم من حيث لا يعلمون﴾ [الأعرَاف: 182]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene atsutsa zivumbulutso zathu, tiwalekelera pang’onopang’ono, kenako nkuwakhaulitsa kuchokera momwe iwo sakudziwa |