Quran with Chichewa translation - Surah Al-Muzzammil ayat 7 - المُزمل - Page - Juz 29
﴿إِنَّ لَكَ فِي ٱلنَّهَارِ سَبۡحٗا طَوِيلٗا ﴾ 
[المُزمل: 7]
﴿إن لك في النهار سبحا طويلا﴾ [المُزمل: 7]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndithu masana uli ndi zochitachita zambiri; (umatanganidwa ndi ntchito yauthenga; dzipatse danga usiku polimbika kupemphera) |