Quran with Chichewa translation - Surah An-Naba’ ayat 18 - النَّبَإ - Page - Juz 30
﴿يَوۡمَ يُنفَخُ فِي ٱلصُّورِ فَتَأۡتُونَ أَفۡوَاجٗا ﴾
[النَّبَإ: 18]
﴿يوم ينفخ في الصور فتأتون أفواجا﴾ [النَّبَإ: 18]
Khaled Ibrahim Betala “Tsiku limene lipenga (lakuuka) lidzaimbidwa ndipo inu mudzabwera (kubwalo losonkhanirana) muli magulumagulu |