Quran with Chichewa translation - Surah Al-Inshiqaq ayat 10 - الانشِقَاق - Page - Juz 30
﴿وَأَمَّا مَنۡ أُوتِيَ كِتَٰبَهُۥ وَرَآءَ ظَهۡرِهِۦ ﴾
[الانشِقَاق: 10]
﴿وأما من أوتي كتابه وراء ظهره﴾ [الانشِقَاق: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Koma yemwe adzapatsidwe kaundula wa zochita zake chakumanzere kudzera kumbuyo kwa msana wake (chifukwa chomunyoza) |