Quran with Chichewa translation - Surah Al-Inshiqaq ayat 13 - الانشِقَاق - Page - Juz 30
﴿إِنَّهُۥ كَانَ فِيٓ أَهۡلِهِۦ مَسۡرُورًا ﴾
[الانشِقَاق: 13]
﴿إنه كان في أهله مسرورا﴾ [الانشِقَاق: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Kamba kakuti iye adali wokondwa; (kukondwa kwa machimo) pamodzi ndi anthu ake (osaganizira za mathero ake) |