×

Surah Al-Munafiqun in Chichewa

Quran Chichewa ⮕ Surah Munafiqun

Translation of the Meanings of Surah Munafiqun in Chichewa - نيانجا

The Quran in Chichewa - Surah Munafiqun translated into Chichewa, Surah Al-Munafiqun in Chichewa. We provide accurate translation of Surah Munafiqun in Chichewa - نيانجا, Verses 11 - Surah Number 63 - Page 554.

بسم الله الرحمن الرحيم

إِذَا جَاءَكَ الْمُنَافِقُونَ قَالُوا نَشْهَدُ إِنَّكَ لَرَسُولُ اللَّهِ ۗ وَاللَّهُ يَعْلَمُ إِنَّكَ لَرَسُولُهُ وَاللَّهُ يَشْهَدُ إِنَّ الْمُنَافِقِينَ لَكَاذِبُونَ (1)
Pamene anthu a chinyengo amadza kwa iwe amati: “Ife tichitira umboni kuti iwe, ndithudi, ndiwe Mtumwi wa Mulungu. Inde Mulungu amadziwa kuti iwe, ndithudi, ndiwe Mtumwi wake ndipo Mulungu achitira umboni kuti anthu achinyengo, ndithudi, ndi abodza
اتَّخَذُوا أَيْمَانَهُمْ جُنَّةً فَصَدُّوا عَن سَبِيلِ اللَّهِ ۚ إِنَّهُمْ سَاءَ مَا كَانُوا يَعْمَلُونَ (2)
Iwo asandutsa malonjezo awo ngati tchingo. Motero iwo amaletsa anthu ena kuti atsatire njira ya Mulungu. Ndithudi zimene iwo amachita ndi zoipa
ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمْ آمَنُوا ثُمَّ كَفَرُوا فَطُبِعَ عَلَىٰ قُلُوبِهِمْ فَهُمْ لَا يَفْقَهُونَ (3)
Ichi ndi chifukwa chakuti iwo adakhulupirirapoyambandipopambuyopakeadayambanso kusakhulupirira. Motero mitima yawo idatsekedwa ndipo sazindikira china chilichonse
۞ وَإِذَا رَأَيْتَهُمْ تُعْجِبُكَ أَجْسَامُهُمْ ۖ وَإِن يَقُولُوا تَسْمَعْ لِقَوْلِهِمْ ۖ كَأَنَّهُمْ خُشُبٌ مُّسَنَّدَةٌ ۖ يَحْسَبُونَ كُلَّ صَيْحَةٍ عَلَيْهِمْ ۚ هُمُ الْعَدُوُّ فَاحْذَرْهُمْ ۚ قَاتَلَهُمُ اللَّهُ ۖ أَنَّىٰ يُؤْفَكُونَ (4)
Ndipo pamene iwe uwaona, matupi awo amakusangalatsa ndipo pamene iwo alankhula, iwe umamvera zonena zawo. Iwo ali ngati matabwa amene aimikidwa pa chipupa. Iwo amaganiza kuti mawu onse amene amveka amanena za iwo. Iwo ndi adani kotero chenjera nawo. Matemberero a Mulungu akhale pa iwo! Kodi iwo asocheretsedwa bwanji kunjira yoyenera
وَإِذَا قِيلَ لَهُمْ تَعَالَوْا يَسْتَغْفِرْ لَكُمْ رَسُولُ اللَّهِ لَوَّوْا رُءُوسَهُمْ وَرَأَيْتَهُمْ يَصُدُّونَ وَهُم مُّسْتَكْبِرُونَ (5)
Ndipo zikanenedwa kwa iwo kuti: “Bwerani kuti mwina Mtumwi wa Mulungu akupemphereni chikhululukiro kuchokera kwa Mulungu, ” iwo amabwerera m’mbuyo ndipo iwe umawaona ali kutembenuza nkhope zawo mwachipongwe
سَوَاءٌ عَلَيْهِمْ أَسْتَغْفَرْتَ لَهُمْ أَمْ لَمْ تَسْتَغْفِرْ لَهُمْ لَن يَغْفِرَ اللَّهُ لَهُمْ ۚ إِنَّ اللَّهَ لَا يَهْدِي الْقَوْمَ الْفَاسِقِينَ (6)
Ndi chimodzimodzi kwa iwo kaya iwe uwapemphera chikhululukiro kapena ayi Mulungu sadzawakhululukira Al Munafiqun 601 iwo. Ndithudi Mulungu satsogolera anthu ophwanya malamulo
هُمُ الَّذِينَ يَقُولُونَ لَا تُنفِقُوا عَلَىٰ مَنْ عِندَ رَسُولِ اللَّهِ حَتَّىٰ يَنفَضُّوا ۗ وَلِلَّهِ خَزَائِنُ السَّمَاوَاتِ وَالْأَرْضِ وَلَٰكِنَّ الْمُنَافِقِينَ لَا يَفْقَهُونَ (7)
Iwo ndiwo amene amati: “Musawapatse china chilichonse anthu amene ali ndi Mtumwi wa Mulungu kuti amuthawe.” Koma Mulungu ndiye Mwini wa chuma cha mlengalenga ndi padziko lapansi koma anthu achinyengo sadziwa zimenezi
يَقُولُونَ لَئِن رَّجَعْنَا إِلَى الْمَدِينَةِ لَيُخْرِجَنَّ الْأَعَزُّ مِنْهَا الْأَذَلَّ ۚ وَلِلَّهِ الْعِزَّةُ وَلِرَسُولِهِ وَلِلْمُؤْمِنِينَ وَلَٰكِنَّ الْمُنَافِقِينَ لَا يَعْلَمُونَ (8)
Iwo amati: “Ngati tibwerera ku Medina, ndithudi, anthu a mphamvu, adzathamangitsa anthu kuchoka ku Mzindawo.” Koma ulemu, mphamvu ndi ulemerero ndi wa Mulungu, Mtumwi wake ndi okhulupilira koma anthu a chinyengo sadziwa chimenechi
يَا أَيُّهَا الَّذِينَ آمَنُوا لَا تُلْهِكُمْ أَمْوَالُكُمْ وَلَا أَوْلَادُكُمْ عَن ذِكْرِ اللَّهِ ۚ وَمَن يَفْعَلْ ذَٰلِكَ فَأُولَٰئِكَ هُمُ الْخَاسِرُونَ (9)
oh inu okhulupirira! Musalole chuma kapena ana anu kuti akusokonezeni pokukumbukira Mulungu. Ndipo aliyense amene achita motero, ndithudi, ndi wotayika
وَأَنفِقُوا مِن مَّا رَزَقْنَاكُم مِّن قَبْلِ أَن يَأْتِيَ أَحَدَكُمُ الْمَوْتُ فَيَقُولَ رَبِّ لَوْلَا أَخَّرْتَنِي إِلَىٰ أَجَلٍ قَرِيبٍ فَأَصَّدَّقَ وَأَكُن مِّنَ الصَّالِحِينَ (10)
Ndipo perekani kuchokera ku katundu amene takupatsani imfa isanadze pa wina wa inu kuti iye asanene kuti: “Oh Ambuye wanga! Inu mukadandibweza mwa kanthawi kochepa, ine ndikadapereka chaulere chochuluka kuchokera ku chuma changa ndikukhala mmodzi wa anthu ochita zabwino.”
وَلَن يُؤَخِّرَ اللَّهُ نَفْسًا إِذَا جَاءَ أَجَلُهَا ۚ وَاللَّهُ خَبِيرٌ بِمَا تَعْمَلُونَ (11)
Ndipo Mulungu sapereka nthawi kwa wina pamene nthawi yake itakwana. Ndipo Mulungu amadziwa chilichonse chimene mumachita
❮ Previous Next ❯

Surahs from Quran :

1- Fatiha2- Baqarah
3- Al Imran4- Nisa
5- Maidah6- Anam
7- Araf8- Anfal
9- Tawbah10- Yunus
11- Hud12- Yusuf
13- Raad14- Ibrahim
15- Hijr16- Nahl
17- Al Isra18- Kahf
19- Maryam20- TaHa
21- Anbiya22- Hajj
23- Muminun24- An Nur
25- Furqan26- Shuara
27- Naml28- Qasas
29- Ankabut30- Rum
31- Luqman32- Sajdah
33- Ahzab34- Saba
35- Fatir36- Yasin
37- Assaaffat38- Sad
39- Zumar40- Ghafir
41- Fussilat42- shura
43- Zukhruf44- Ad Dukhaan
45- Jathiyah46- Ahqaf
47- Muhammad48- Al Fath
49- Hujurat50- Qaf
51- zariyat52- Tur
53- Najm54- Al Qamar
55- Rahman56- Waqiah
57- Hadid58- Mujadilah
59- Al Hashr60- Mumtahina
61- Saff62- Jumuah
63- Munafiqun64- Taghabun
65- Talaq66- Tahrim
67- Mulk68- Qalam
69- Al-Haqqah70- Maarij
71- Nuh72- Jinn
73- Muzammil74- Muddathir
75- Qiyamah76- Insan
77- Mursalat78- An Naba
79- Naziat80- Abasa
81- Takwir82- Infitar
83- Mutaffifin84- Inshiqaq
85- Buruj86- Tariq
87- Al Ala88- Ghashiya
89- Fajr90- Al Balad
91- Shams92- Lail
93- Duha94- Sharh
95- Tin96- Al Alaq
97- Qadr98- Bayyinah
99- Zalzalah100- Adiyat
101- Qariah102- Takathur
103- Al Asr104- Humazah
105- Al Fil106- Quraysh
107- Maun108- Kawthar
109- Kafirun110- Nasr
111- Masad112- Ikhlas
113- Falaq114- An Nas