×

Pamene anthu a chinyengo amadza kwa iwe amati: “Ife tichitira umboni kuti 63:1 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Munafiqun ⮕ (63:1) ayat 1 in Chichewa

63:1 Surah Al-Munafiqun ayat 1 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Munafiqun ayat 1 - المُنَافِقُونَ - Page - Juz 28

﴿إِذَا جَآءَكَ ٱلۡمُنَٰفِقُونَ قَالُواْ نَشۡهَدُ إِنَّكَ لَرَسُولُ ٱللَّهِۗ وَٱللَّهُ يَعۡلَمُ إِنَّكَ لَرَسُولُهُۥ وَٱللَّهُ يَشۡهَدُ إِنَّ ٱلۡمُنَٰفِقِينَ لَكَٰذِبُونَ ﴾
[المُنَافِقُونَ: 1]

Pamene anthu a chinyengo amadza kwa iwe amati: “Ife tichitira umboni kuti iwe, ndithudi, ndiwe Mtumwi wa Mulungu. Inde Mulungu amadziwa kuti iwe, ndithudi, ndiwe Mtumwi wake ndipo Mulungu achitira umboni kuti anthu achinyengo, ndithudi, ndi abodza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إذا جاءك المنافقون قالوا نشهد إنك لرسول الله والله يعلم إنك لرسوله, باللغة نيانجا

﴿إذا جاءك المنافقون قالوا نشهد إنك لرسول الله والله يعلم إنك لرسوله﴾ [المُنَافِقُونَ: 1]

Khaled Ibrahim Betala
“Akakudzera achiphamaso akunena kuti: “Tikuikira umboni kuti ndithu iwe ndiwe Mtumiki wa Allah, ndipo Allah akudziwa kuti iwe ndiwe mtumiki Wake. Ndipo Allah akuikira umboni kuti achiphamaso ngabodza (pa zomwe akunena)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek