×

Ndipo pamene iwe uwaona, matupi awo amakusangalatsa ndipo pamene iwo alankhula, iwe 63:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Munafiqun ⮕ (63:4) ayat 4 in Chichewa

63:4 Surah Al-Munafiqun ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Munafiqun ayat 4 - المُنَافِقُونَ - Page - Juz 28

﴿۞ وَإِذَا رَأَيۡتَهُمۡ تُعۡجِبُكَ أَجۡسَامُهُمۡۖ وَإِن يَقُولُواْ تَسۡمَعۡ لِقَوۡلِهِمۡۖ كَأَنَّهُمۡ خُشُبٞ مُّسَنَّدَةٞۖ يَحۡسَبُونَ كُلَّ صَيۡحَةٍ عَلَيۡهِمۡۚ هُمُ ٱلۡعَدُوُّ فَٱحۡذَرۡهُمۡۚ قَٰتَلَهُمُ ٱللَّهُۖ أَنَّىٰ يُؤۡفَكُونَ ﴾
[المُنَافِقُونَ: 4]

Ndipo pamene iwe uwaona, matupi awo amakusangalatsa ndipo pamene iwo alankhula, iwe umamvera zonena zawo. Iwo ali ngati matabwa amene aimikidwa pa chipupa. Iwo amaganiza kuti mawu onse amene amveka amanena za iwo. Iwo ndi adani kotero chenjera nawo. Matemberero a Mulungu akhale pa iwo! Kodi iwo asocheretsedwa bwanji kunjira yoyenera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا رأيتهم تعجبك أجسامهم وإن يقولوا تسمع لقولهم كأنهم خشب مسندة يحسبون, باللغة نيانجا

﴿وإذا رأيتهم تعجبك أجسامهم وإن يقولوا تسمع لقولهم كأنهم خشب مسندة يحسبون﴾ [المُنَافِقُونَ: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ukawaona, akukondweretsa matupi awo; ndipo akayankhula umvetsera zoyankhula zawo (chifukwa chakuthwa kwa malirime awo, pomwe mkati mwawo ndiming’oma yopanda kanthu); iwo ali ngati matsinde a mitengo yomwe yayadzamiritsidwa (ku chipupa); (mwa iwo mulibe moyo). Mkuwe uliwonse (umene akuumva) akuganiza kuti ukulinga iwo, (chifukwa cha kuzindikira chinyengo chawo); iwowa ndiadani; chenjerani nawo. Allah awatembelere! Mwanjira yanji akuchotsedwa (ku choonadi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek