×

Iwo asandutsa malonjezo awo ngati tchingo. Motero iwo amaletsa anthu ena kuti 63:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Munafiqun ⮕ (63:2) ayat 2 in Chichewa

63:2 Surah Al-Munafiqun ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Munafiqun ayat 2 - المُنَافِقُونَ - Page - Juz 28

﴿ٱتَّخَذُوٓاْ أَيۡمَٰنَهُمۡ جُنَّةٗ فَصَدُّواْ عَن سَبِيلِ ٱللَّهِۚ إِنَّهُمۡ سَآءَ مَا كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[المُنَافِقُونَ: 2]

Iwo asandutsa malonjezo awo ngati tchingo. Motero iwo amaletsa anthu ena kuti atsatire njira ya Mulungu. Ndithudi zimene iwo amachita ndi zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: اتخذوا أيمانهم جنة فصدوا عن سبيل الله إنهم ساء ما كانوا يعملون, باللغة نيانجا

﴿اتخذوا أيمانهم جنة فصدوا عن سبيل الله إنهم ساء ما كانوا يعملون﴾ [المُنَافِقُونَ: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“Kulumbira kwawo (kwa bodza) akuchita kukhala chotetezera (chuma chawo ndi matupi awo). Tero atsekereza (anthu kuyenda) panjira ya Allah. Ndithu nzoipa zedi zimene amachita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek