×

Ndi chimodzimodzi kwa iwo kaya iwe uwapemphera chikhululukiro kapena ayi Mulungu sadzawakhululukira 63:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Munafiqun ⮕ (63:6) ayat 6 in Chichewa

63:6 Surah Al-Munafiqun ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Munafiqun ayat 6 - المُنَافِقُونَ - Page - Juz 28

﴿سَوَآءٌ عَلَيۡهِمۡ أَسۡتَغۡفَرۡتَ لَهُمۡ أَمۡ لَمۡ تَسۡتَغۡفِرۡ لَهُمۡ لَن يَغۡفِرَ ٱللَّهُ لَهُمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ لَا يَهۡدِي ٱلۡقَوۡمَ ٱلۡفَٰسِقِينَ ﴾
[المُنَافِقُونَ: 6]

Ndi chimodzimodzi kwa iwo kaya iwe uwapemphera chikhululukiro kapena ayi Mulungu sadzawakhululukira Al Munafiqun 601 iwo. Ndithudi Mulungu satsogolera anthu ophwanya malamulo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: سواء عليهم أستغفرت لهم أم لم تستغفر لهم لن يغفر الله لهم, باللغة نيانجا

﴿سواء عليهم أستغفرت لهم أم لم تستغفر لهم لن يغفر الله لهم﴾ [المُنَافِقُونَ: 6]

Khaled Ibrahim Betala
“Kwa iwowa nchimodzimodzi kuwapemphera kwako chikhululuko, kapena kusawapemphera. Allah sangawakhululukire (chifukwa cha kuzama kwawo m’kusakhulupirira). Ndithu Allah saongola anthu otuluka m’chilamulo (Chake)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek