×

Ndipo zikanenedwa kwa iwo kuti: “Bwerani kuti mwina Mtumwi wa Mulungu akupemphereni 63:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Munafiqun ⮕ (63:5) ayat 5 in Chichewa

63:5 Surah Al-Munafiqun ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Munafiqun ayat 5 - المُنَافِقُونَ - Page - Juz 28

﴿وَإِذَا قِيلَ لَهُمۡ تَعَالَوۡاْ يَسۡتَغۡفِرۡ لَكُمۡ رَسُولُ ٱللَّهِ لَوَّوۡاْ رُءُوسَهُمۡ وَرَأَيۡتَهُمۡ يَصُدُّونَ وَهُم مُّسۡتَكۡبِرُونَ ﴾
[المُنَافِقُونَ: 5]

Ndipo zikanenedwa kwa iwo kuti: “Bwerani kuti mwina Mtumwi wa Mulungu akupemphereni chikhululukiro kuchokera kwa Mulungu, ” iwo amabwerera m’mbuyo ndipo iwe umawaona ali kutembenuza nkhope zawo mwachipongwe

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا قيل لهم تعالوا يستغفر لكم رسول الله لووا رءوسهم ورأيتهم يصدون, باللغة نيانجا

﴿وإذا قيل لهم تعالوا يستغفر لكم رسول الله لووا رءوسهم ورأيتهم يصدون﴾ [المُنَافِقُونَ: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Kukanenedwa kwa iwo kuti: “Bwerani, akupemphereni chikhululuko mthenga wa Allah, akutembenuza mitu yawo (monyoza ndi modzitukumula), ndipo uwaona akunyoza uku akudzikweza (osatsatira langizo).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek