Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 14 - يُونس - Page - Juz 11
﴿ثُمَّ جَعَلۡنَٰكُمۡ خَلَٰٓئِفَ فِي ٱلۡأَرۡضِ مِنۢ بَعۡدِهِمۡ لِنَنظُرَ كَيۡفَ تَعۡمَلُونَ ﴾
[يُونس: 14]
﴿ثم جعلناكم خلائف في الأرض من بعدهم لننظر كيف تعملون﴾ [يُونس: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Kenako takupangani inu (Asilamu) kukhala olowa m’malo mwawo pa dziko pambuyo pawo kuti tione mmene mungachitire (zabwino kapena zoipa) |