Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 13 - يُونس - Page - Juz 11
﴿وَلَقَدۡ أَهۡلَكۡنَا ٱلۡقُرُونَ مِن قَبۡلِكُمۡ لَمَّا ظَلَمُواْ وَجَآءَتۡهُمۡ رُسُلُهُم بِٱلۡبَيِّنَٰتِ وَمَا كَانُواْ لِيُؤۡمِنُواْۚ كَذَٰلِكَ نَجۡزِي ٱلۡقَوۡمَ ٱلۡمُجۡرِمِينَ ﴾
[يُونس: 13]
﴿ولقد أهلكنا القرون من قبلكم لما ظلموا وجاءتهم رسلهم بالبينات وما كانوا﴾ [يُونس: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu tidaiononga mibadwo yambiri patsogolo panu pamene idachita zoipa. Komatu atumiki awo adawadzera ndi zisonyezo zoonekera, koma sadali oti nkukhulupirira. Umo ndi momwenso tidzawalipire anthu ochita zoipa |