Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 51 - يُونس - Page - Juz 11
﴿أَثُمَّ إِذَا مَا وَقَعَ ءَامَنتُم بِهِۦٓۚ ءَآلۡـَٰٔنَ وَقَدۡ كُنتُم بِهِۦ تَسۡتَعۡجِلُونَ ﴾
[يُونس: 51]
﴿أثم إذا ما وقع آمنتم به آلآن وقد كنتم به تستعجلون﴾ [يُونس: 51]
Khaled Ibrahim Betala (““Kodi chikadza ndipamene mudzachikhulupirire?” Panthawiyo mudzauzidwa): “Kodi tsopano (ndi pamene mukukhulupirira), chikhalirecho mudali kuchifulumizitsa (kale)?” |