×

Ndithudi iwo amene akhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, Ambuye wawo adzawatsogolera m’chikhulupiriro 10:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yunus ⮕ (10:9) ayat 9 in Chichewa

10:9 Surah Yunus ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 9 - يُونس - Page - Juz 11

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ يَهۡدِيهِمۡ رَبُّهُم بِإِيمَٰنِهِمۡۖ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهِمُ ٱلۡأَنۡهَٰرُ فِي جَنَّٰتِ ٱلنَّعِيمِ ﴾
[يُونس: 9]

Ndithudi iwo amene akhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, Ambuye wawo adzawatsogolera m’chikhulupiriro chawo. Mitsinje idzakhala ili kuyenda pansi pawo m’minda ya mtendere

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين آمنوا وعملوا الصالحات يهديهم ربهم بإيمانهم تجري من تحتهم الأنهار, باللغة نيانجا

﴿إن الذين آمنوا وعملوا الصالحات يهديهم ربهم بإيمانهم تجري من تحتهم الأنهار﴾ [يُونس: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene akhulupirira ndi kumachita zabwino, Mbuye wawo awaongola chifukwa cha chikhulupiliro chawo. Pansi (ndi patsogolo) pawo mitsinje ikuyenda m’Minda yamtendere
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek