×

“Ndiponso ulangizi wanga siudzakuthandizani ngakhale nditafuna kukulangizani ngati chifuniro cha Mulungu ndi 11:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Hud ⮕ (11:34) ayat 34 in Chichewa

11:34 Surah Hud ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 34 - هُود - Page - Juz 12

﴿وَلَا يَنفَعُكُمۡ نُصۡحِيٓ إِنۡ أَرَدتُّ أَنۡ أَنصَحَ لَكُمۡ إِن كَانَ ٱللَّهُ يُرِيدُ أَن يُغۡوِيَكُمۡۚ هُوَ رَبُّكُمۡ وَإِلَيۡهِ تُرۡجَعُونَ ﴾
[هُود: 34]

“Ndiponso ulangizi wanga siudzakuthandizani ngakhale nditafuna kukulangizani ngati chifuniro cha Mulungu ndi kukusocheretsani. Iye ndi Ambuye wanu ndipo ndi kwa Iye mudzabwerera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا ينفعكم نصحي إن أردت أن أنصح لكم إن كان الله يريد, باللغة نيانجا

﴿ولا ينفعكم نصحي إن أردت أن أنصح لكم إن كان الله يريد﴾ [هُود: 34]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo kulangiza kwanga sikungakuthandizeni ngati ntafuna kukulangizani, ngati Allah akufuna kukulekelerani kusokera. Iye ndiye Mbuye wanu. Ndipo kwa Iye mudzabwezedwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek