×

“Kotero Ambuye wako adzakusankha iwe ndikukuphunzitsa kutathauzira maloto ndi kukwaniritsa chisomo chake 12:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:6) ayat 6 in Chichewa

12:6 Surah Yusuf ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 6 - يُوسُف - Page - Juz 12

﴿وَكَذَٰلِكَ يَجۡتَبِيكَ رَبُّكَ وَيُعَلِّمُكَ مِن تَأۡوِيلِ ٱلۡأَحَادِيثِ وَيُتِمُّ نِعۡمَتَهُۥ عَلَيۡكَ وَعَلَىٰٓ ءَالِ يَعۡقُوبَ كَمَآ أَتَمَّهَا عَلَىٰٓ أَبَوَيۡكَ مِن قَبۡلُ إِبۡرَٰهِيمَ وَإِسۡحَٰقَۚ إِنَّ رَبَّكَ عَلِيمٌ حَكِيمٞ ﴾
[يُوسُف: 6]

“Kotero Ambuye wako adzakusankha iwe ndikukuphunzitsa kutathauzira maloto ndi kukwaniritsa chisomo chake pa iwe ndiponso kwa ana a Yakobo, monga momwe adakwaniritsira kwa makolo ako Abrahamu ndi Isake kale! Ndithudi Ambuye wako ndi wodziwa zilizonse ndi Wanzeru.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكذلك يجتبيك ربك ويعلمك من تأويل الأحاديث ويتم نعمته عليك وعلى آل, باللغة نيانجا

﴿وكذلك يجتبيك ربك ويعلمك من تأويل الأحاديث ويتم نعمته عليك وعلى آل﴾ [يُوسُف: 6]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo momwemo Mbuye wako akusankha komanso akuphunzitsa kumasulira nkhani (za maloto) ndi kukwaniritsa mtendere Wake pa iwe, ndi pa mbumba ya Ya’qub monga momwe adakwaniritsira kwa makolo ako kale, Ibrahim ndi Ishaq. Ndithu Mbuye wako Ngodziwa, Ngwanzeru zakuya.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek