×

Iye adati, “Ine ndidzakupempherani chikhululukiro kwa Ambuye wanga. Ndithudi Iye ndi wokhululukira 12:98 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:98) ayat 98 in Chichewa

12:98 Surah Yusuf ayat 98 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 98 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿قَالَ سَوۡفَ أَسۡتَغۡفِرُ لَكُمۡ رَبِّيٓۖ إِنَّهُۥ هُوَ ٱلۡغَفُورُ ٱلرَّحِيمُ ﴾
[يُوسُف: 98]

Iye adati, “Ine ndidzakupempherani chikhululukiro kwa Ambuye wanga. Ndithudi Iye ndi wokhululukira ndiponso ndi Wachisoni chosatha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال سوف أستغفر لكم ربي إنه هو الغفور الرحيم, باللغة نيانجا

﴿قال سوف أستغفر لكم ربي إنه هو الغفور الرحيم﴾ [يُوسُف: 98]

Khaled Ibrahim Betala
“(Iye) adati: “Posachedwapa (ndikamuona Yûsuf) ndikupempherani chikhululuko kwa Mbuye wanga. Ndithu Iye Ngokhululuka zedi, Ngwachisoni chosatha.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek