Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 88 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿لَا تَمُدَّنَّ عَيۡنَيۡكَ إِلَىٰ مَا مَتَّعۡنَا بِهِۦٓ أَزۡوَٰجٗا مِّنۡهُمۡ وَلَا تَحۡزَنۡ عَلَيۡهِمۡ وَٱخۡفِضۡ جَنَاحَكَ لِلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[الحِجر: 88]
﴿لا تمدن عينيك إلى ما متعنا به أزواجا منهم ولا تحزن عليهم﴾ [الحِجر: 88]
Khaled Ibrahim Betala “Usatong’olere maso ako (kuyang’ana) zimene tawasangalatsa nazo mitundumitundu ya mwa iwo (monga chuma cha anthu osakhulupirira). Usawadandaulirenso iwo ndipo tsitsa phiko lako kwa okhululupirira, (uwafungatire) |