Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 10 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿هُوَ ٱلَّذِيٓ أَنزَلَ مِنَ ٱلسَّمَآءِ مَآءٗۖ لَّكُم مِّنۡهُ شَرَابٞ وَمِنۡهُ شَجَرٞ فِيهِ تُسِيمُونَ ﴾
[النَّحل: 10]
﴿هو الذي أنـزل من السماء ماء لكم منه شراب ومنه شجر فيه﴾ [النَّحل: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Iye ndi Amene akukutsitsirani madzi kuchokera ku mitambo, madziwo mumamwa (pothetsa ludzu lanu), ndipo ndi madziwo mitengo imamera; mitengo yomwe mumadyetsera ziweto (zanu) |