×

Zili kwa Mulungu kusonyeza njira yoyenera, koma pali njirazinazopatukandipo Iyeakadafunaakadakutsogolerani nonse 16:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:9) ayat 9 in Chichewa

16:9 Surah An-Nahl ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 9 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَعَلَى ٱللَّهِ قَصۡدُ ٱلسَّبِيلِ وَمِنۡهَا جَآئِرٞۚ وَلَوۡ شَآءَ لَهَدَىٰكُمۡ أَجۡمَعِينَ ﴾
[النَّحل: 9]

Zili kwa Mulungu kusonyeza njira yoyenera, koma pali njirazinazopatukandipo Iyeakadafunaakadakutsogolerani nonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وعلى الله قصد السبيل ومنها جائر ولو شاء لهداكم أجمعين, باللغة نيانجا

﴿وعلى الله قصد السبيل ومنها جائر ولو شاء لهداكم أجمعين﴾ [النَّحل: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndi udindo wa Allah kusonyeza njira yolungama (yomwe ingakufikitseni ku Munda wamtendere), koma zilipo njira zina zokhota (zomwe sizifikitsa ku choonadi). Ndipo Allah akadafuna, akadakuongolani nonsenu (mwa chifuniro chanu ndi mopanda chifuniro chanu. Koma Iye adakupatsani nzeru kuti musankhe nokha njira imene mufuna)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek