Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 17 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿أَفَمَن يَخۡلُقُ كَمَن لَّا يَخۡلُقُۚ أَفَلَا تَذَكَّرُونَ ﴾
[النَّحل: 17]
﴿أفمن يخلق كمن لا يخلق أفلا تذكرون﴾ [النَّحل: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi Yemwe amalenga angalingane ndi omwe salenga? Kodi simungakumbukire (ndikudziwa kulakwa kwanu pomuyerekeza Allah ndi mafano) |