Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 16 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿وَعَلَٰمَٰتٖۚ وَبِٱلنَّجۡمِ هُمۡ يَهۡتَدُونَ ﴾ 
[النَّحل: 16]
﴿وعلامات وبالنجم هم يهتدون﴾ [النَّحل: 16]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (adaikanso) zizindikiro zina, ndiponso kupyolera m’nyenyezi, iwo amalondola njira |