×

Ndipo kuchokera ku zipatso za mitengo ya tende ndi mitengo ya mphesa, 16:67 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:67) ayat 67 in Chichewa

16:67 Surah An-Nahl ayat 67 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 67 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَمِن ثَمَرَٰتِ ٱلنَّخِيلِ وَٱلۡأَعۡنَٰبِ تَتَّخِذُونَ مِنۡهُ سَكَرٗا وَرِزۡقًا حَسَنًاۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَةٗ لِّقَوۡمٖ يَعۡقِلُونَ ﴾
[النَّحل: 67]

Ndipo kuchokera ku zipatso za mitengo ya tende ndi mitengo ya mphesa, inu mumapanga zakumwa zoledzeretsa ndiponso chakudya chabwino. Ndithudi mu zimenezi muli zizindikiro kwa anthu amene ali ndi nzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن ثمرات النخيل والأعناب تتخذون منه سكرا ورزقا حسنا إن في ذلك, باللغة نيانجا

﴿ومن ثمرات النخيل والأعناب تتخذون منه سكرا ورزقا حسنا إن في ذلك﴾ [النَّحل: 67]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kuchokera ku zipatso za tende ndi mphesa, mumakonza zakumwa zoledzeretsa (zomwe nzoletsedwa) ndikupezanso rizq labwino (m’zipatsozo); ndithudi m’zimenezo muli lingaliro kwa anthu oganiza mwanzeru
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek