×

Ndipo iwo amapembedza mafano mowonjezera pa Mulungu amene sangathe kuwapatsa chithandizo chilichonse 16:73 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:73) ayat 73 in Chichewa

16:73 Surah An-Nahl ayat 73 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 73 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَيَعۡبُدُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ مَا لَا يَمۡلِكُ لَهُمۡ رِزۡقٗا مِّنَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ شَيۡـٔٗا وَلَا يَسۡتَطِيعُونَ ﴾
[النَّحل: 73]

Ndipo iwo amapembedza mafano mowonjezera pa Mulungu amene sangathe kuwapatsa chithandizo chilichonse kuchokera kumwamba kapena padziko lapansi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويعبدون من دون الله ما لا يملك لهم رزقا من السموات والأرض, باللغة نيانجا

﴿ويعبدون من دون الله ما لا يملك لهم رزقا من السموات والأرض﴾ [النَّحل: 73]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akumusiya Allah ndikupembedza zomwe sizingawapezere zopatsa ngakhale pang’ono, zochokera kumwamba ndi pansi ndipo sizikhoza chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek