×

Ulemerero ukhale kwa Iye amene adayendetsa kapolo wake nthawi ya usiku kuchoka 17:1 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:1) ayat 1 in Chichewa

17:1 Surah Al-Isra’ ayat 1 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 1 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿سُبۡحَٰنَ ٱلَّذِيٓ أَسۡرَىٰ بِعَبۡدِهِۦ لَيۡلٗا مِّنَ ٱلۡمَسۡجِدِ ٱلۡحَرَامِ إِلَى ٱلۡمَسۡجِدِ ٱلۡأَقۡصَا ٱلَّذِي بَٰرَكۡنَا حَوۡلَهُۥ لِنُرِيَهُۥ مِنۡ ءَايَٰتِنَآۚ إِنَّهُۥ هُوَ ٱلسَّمِيعُ ٱلۡبَصِيرُ ﴾
[الإسرَاء: 1]

Ulemerero ukhale kwa Iye amene adayendetsa kapolo wake nthawi ya usiku kuchoka ku Mzikiti Wolemekezeka kupita ku Mzikiti wakutali umene malo ake ozungulira tidawadalitsa; kuti timuonetse zina za zizindikiro zathu. Ndithudi Iye ndiwakumva ndipo woona zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: سبحان الذي أسرى بعبده ليلا من المسجد الحرام إلى المسجد الأقصى الذي, باللغة نيانجا

﴿سبحان الذي أسرى بعبده ليلا من المسجد الحرام إلى المسجد الأقصى الذي﴾ [الإسرَاء: 1]

Khaled Ibrahim Betala
“۞ Ulemelero ngwa Yemwe adayendetsa kapolo Wake usiku (umodzi) kuchokera mu Msikiti Wopatulika (wa Makka) kupita ku Msikiti wakutali (wa Baitul-Muqaddas), womwe tidazidalitsa zomwe zauzungulira. (Tidampititsa kumeneko) kuti timsonyeze zina mwa zisonyezo Zathu; ndithu Iye (Allah) Ngwakumva, Ngowona ( chilichonse)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek