×

Ndipo Ambuye wako walamula kuti musapembedze wina aliyense koma Iye yekha. Ndipo 17:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:23) ayat 23 in Chichewa

17:23 Surah Al-Isra’ ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 23 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿۞ وَقَضَىٰ رَبُّكَ أَلَّا تَعۡبُدُوٓاْ إِلَّآ إِيَّاهُ وَبِٱلۡوَٰلِدَيۡنِ إِحۡسَٰنًاۚ إِمَّا يَبۡلُغَنَّ عِندَكَ ٱلۡكِبَرَ أَحَدُهُمَآ أَوۡ كِلَاهُمَا فَلَا تَقُل لَّهُمَآ أُفّٖ وَلَا تَنۡهَرۡهُمَا وَقُل لَّهُمَا قَوۡلٗا كَرِيمٗا ﴾
[الإسرَاء: 23]

Ndipo Ambuye wako walamula kuti musapembedze wina aliyense koma Iye yekha. Ndipo kuti muwachitire makolo anu zabwino. Ngati wina wa iwo kapena onse akalamba ali kukhala nanu, musawakalipire ayi, koma muziwayankhula ndi mawu aulemu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقضى ربك ألا تعبدوا إلا إياه وبالوالدين إحسانا إما يبلغن عندك الكبر, باللغة نيانجا

﴿وقضى ربك ألا تعبدوا إلا إياه وبالوالدين إحسانا إما يبلغن عندك الكبر﴾ [الإسرَاء: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo walamula Mbuye wako kuti musapembedze (wina) koma Iye Yekha, ndi kuti muchitire zabwino makolo (anu). Ngati m’modzi wa iwo afika msinkhu waukalamba uli naye, kapena onse awiri, usawanenere mawu amnyozo, ndiponso usawakalipire koma yankhula nawo ndi mau aulemu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek