×

Lolungama kuti lichenjeze za chilango chowawa chochokera kwa Iye ndi kuwauza anthu 18:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:2) ayat 2 in Chichewa

18:2 Surah Al-Kahf ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 2 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿قَيِّمٗا لِّيُنذِرَ بَأۡسٗا شَدِيدٗا مِّن لَّدُنۡهُ وَيُبَشِّرَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ٱلَّذِينَ يَعۡمَلُونَ ٱلصَّٰلِحَٰتِ أَنَّ لَهُمۡ أَجۡرًا حَسَنٗا ﴾
[الكَهف: 2]

Lolungama kuti lichenjeze za chilango chowawa chochokera kwa Iye ndi kuwauza anthu okhulupirira amene amachita ntchito zabwino kuti adzalandira mphotho yabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قيما لينذر بأسا شديدا من لدنه ويبشر المؤمنين الذين يعملون الصالحات أن, باللغة نيانجا

﴿قيما لينذر بأسا شديدا من لدنه ويبشر المؤمنين الذين يعملون الصالحات أن﴾ [الكَهف: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“(Walichita kukhala) loongoka kuti lichenjeze anthu za chilango chokhwima chochokera kwa Iye (Allah), ndikuti liwasangalatse okhulupirira omwe akuchita zabwino, kuti adzapeza malipiro abwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek