Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 1 - الكَهف - Page - Juz 15
﴿ٱلۡحَمۡدُ لِلَّهِ ٱلَّذِيٓ أَنزَلَ عَلَىٰ عَبۡدِهِ ٱلۡكِتَٰبَ وَلَمۡ يَجۡعَل لَّهُۥ عِوَجَاۜ ﴾
[الكَهف: 1]
﴿الحمد لله الذي أنـزل على عبده الكتاب ولم يجعل له عوجا﴾ [الكَهف: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Kutamandidwa konse kwabwino nkwa Allah, Yemwe adavumbulutsa kwa kapolo Wake (Mtumiki Muhammad{s.a.w}), buku (ili lopatulika), ndipo sadalikhotetse (koma m’menemo muli zoona zokhazokha) |