Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 15 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَسَلَٰمٌ عَلَيۡهِ يَوۡمَ وُلِدَ وَيَوۡمَ يَمُوتُ وَيَوۡمَ يُبۡعَثُ حَيّٗا ﴾
[مَريَم: 15]
﴿وسلام عليه يوم ولد ويوم يموت ويوم يبعث حيا﴾ [مَريَم: 15]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo mtendere wa Allah udali pa iye kuyambira tsiku lomwe adabadwa ndi tsiku lomwe adamwalira, ndi tsiku limene adzaukitsidwa ku imfa kukhala wamoyo |