Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 74 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَكَمۡ أَهۡلَكۡنَا قَبۡلَهُم مِّن قَرۡنٍ هُمۡ أَحۡسَنُ أَثَٰثٗا وَرِءۡيٗا ﴾
[مَريَم: 74]
﴿وكم أهلكنا قبلهم من قرن هم أحسن أثاثا ورئيا﴾ [مَريَم: 74]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo mibadwo yambiri tidaiononga patsogolo pawo, yomwe idali ndi ziwiya zabwino ndi maonekedwe abwino |