Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 80 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَنَرِثُهُۥ مَا يَقُولُ وَيَأۡتِينَا فَرۡدٗا ﴾
[مَريَم: 80]
﴿ونرثه ما يقول ويأتينا فردا﴾ [مَريَم: 80]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidzamlowa mmalo zimene akunenazi, (chuma ndi anawo), nadzatidzera ali yekhayekha (wopanda chuma ndi zonse zomwe ankanyadira) |