×

Kodi kapena inu mukunena kuti Abrahamu, Ishimayeli, Isake, Yakobo ndi mitundu yake 2:140 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:140) ayat 140 in Chichewa

2:140 Surah Al-Baqarah ayat 140 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 140 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿أَمۡ تَقُولُونَ إِنَّ إِبۡرَٰهِـۧمَ وَإِسۡمَٰعِيلَ وَإِسۡحَٰقَ وَيَعۡقُوبَ وَٱلۡأَسۡبَاطَ كَانُواْ هُودًا أَوۡ نَصَٰرَىٰۗ قُلۡ ءَأَنتُمۡ أَعۡلَمُ أَمِ ٱللَّهُۗ وَمَنۡ أَظۡلَمُ مِمَّن كَتَمَ شَهَٰدَةً عِندَهُۥ مِنَ ٱللَّهِۗ وَمَا ٱللَّهُ بِغَٰفِلٍ عَمَّا تَعۡمَلُونَ ﴾
[البَقَرَة: 140]

Kodi kapena inu mukunena kuti Abrahamu, Ishimayeli, Isake, Yakobo ndi mitundu yake adali Ayuda kapena Akhirisitu? Nena: “Kodi inu mumadziwa kapena Mulungu? Kodi oipa kwambiri ndani kuposa munthu amene amabisa mawu amene walandira kuchokera kwa Mulungu? Koma Mulungu saiwala zimene mukuchita.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أم تقولون إن إبراهيم وإسماعيل وإسحاق ويعقوب والأسباط كانوا هودا أو نصارى, باللغة نيانجا

﴿أم تقولون إن إبراهيم وإسماعيل وإسحاق ويعقوب والأسباط كانوا هودا أو نصارى﴾ [البَقَرَة: 140]

Khaled Ibrahim Betala
“Kapena (inu Ayuda) mukunena kuti Ibrahim, Ismail Ishâq, Yaqub ndi zidzukulu anali Ayuda kapena Akhrisitu? Nena: “Kodi inu ndi odziwa kwambiri kapena Allah?” Kodi ndani woipitsitsa koposa yemwe wabisa umboni omwe ali nao ochokera kwa Allah! Komatu Allah sali wonyalanyaza pa zimene mukuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek