Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 152 - البَقَرَة - Page - Juz 2
﴿فَٱذۡكُرُونِيٓ أَذۡكُرۡكُمۡ وَٱشۡكُرُواْ لِي وَلَا تَكۡفُرُونِ ﴾
[البَقَرَة: 152]
﴿فاذكروني أذكركم واشكروا لي ولا تكفرون﴾ [البَقَرَة: 152]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho ndikumbukireni (pondithokoza pa mtendere umene ndakupatsaniwu). Nanenso ndikukumbukirani (pokulipirani mphoto yaikulu). Ndipo ndiyamikeni; musandikane |