×

Ndipo pamene akapolo anga akufunsa za Ine, auze kuti: “Ndithudi Ine ndili 2:186 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:186) ayat 186 in Chichewa

2:186 Surah Al-Baqarah ayat 186 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 186 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿وَإِذَا سَأَلَكَ عِبَادِي عَنِّي فَإِنِّي قَرِيبٌۖ أُجِيبُ دَعۡوَةَ ٱلدَّاعِ إِذَا دَعَانِۖ فَلۡيَسۡتَجِيبُواْ لِي وَلۡيُؤۡمِنُواْ بِي لَعَلَّهُمۡ يَرۡشُدُونَ ﴾
[البَقَرَة: 186]

Ndipo pamene akapolo anga akufunsa za Ine, auze kuti: “Ndithudi Ine ndili pafupi ndipo ndimayankha pempho la aliyense akandipempha. Motero andimvere Ine ndi kukhulupirira kuti akhoza kuyenda m’njira yoyenera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا سألك عبادي عني فإني قريب أجيب دعوة الداع إذا دعان فليستجيبوا, باللغة نيانجا

﴿وإذا سألك عبادي عني فإني قريب أجيب دعوة الداع إذا دعان فليستجيبوا﴾ [البَقَرَة: 186]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akapolo anga akakufunsa za ine, (auze kuti) Ine ndili pafupi nawo. Ndimayankha zopempha za wopempha pamene akundipempha. Choncho iwo ayankhe kuitana kwanga ndipo andikhulupirire kuti aongoke
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek