×

Kufanana kwa amene amapereka chuma chawo m’njira ya Mulungu kuli ngati njere 2:261 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:261) ayat 261 in Chichewa

2:261 Surah Al-Baqarah ayat 261 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 261 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿مَّثَلُ ٱلَّذِينَ يُنفِقُونَ أَمۡوَٰلَهُمۡ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ كَمَثَلِ حَبَّةٍ أَنۢبَتَتۡ سَبۡعَ سَنَابِلَ فِي كُلِّ سُنۢبُلَةٖ مِّاْئَةُ حَبَّةٖۗ وَٱللَّهُ يُضَٰعِفُ لِمَن يَشَآءُۚ وَٱللَّهُ وَٰسِعٌ عَلِيمٌ ﴾
[البَقَرَة: 261]

Kufanana kwa amene amapereka chuma chawo m’njira ya Mulungu kuli ngati njere ya tirigu imene imabereka njere zina zisanu ndi ziwiri ndipo ililonse imabereka njere zana limodzi. Mulungu amapereka moolowa manja kwa amene wamufuna. Ndipo Mulungu ali ndi zonse zimene zolengedwa zake zimafuna. Iye amadziwa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: مثل الذين ينفقون أموالهم في سبيل الله كمثل حبة أنبتت سبع سنابل, باللغة نيانجا

﴿مثل الذين ينفقون أموالهم في سبيل الله كمثل حبة أنبتت سبع سنابل﴾ [البَقَرَة: 261]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek