×

Mawu abwino ndi chikhululukiro ndi zinthu zabwino kuposa chopereka chaulere chimene chimatsatiridwa 2:263 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:263) ayat 263 in Chichewa

2:263 Surah Al-Baqarah ayat 263 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 263 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿۞ قَوۡلٞ مَّعۡرُوفٞ وَمَغۡفِرَةٌ خَيۡرٞ مِّن صَدَقَةٖ يَتۡبَعُهَآ أَذٗىۗ وَٱللَّهُ غَنِيٌّ حَلِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 263]

Mawu abwino ndi chikhululukiro ndi zinthu zabwino kuposa chopereka chaulere chimene chimatsatiridwa ndi kutafula. Mulungu ndi wolemera ndipo ndi wopirira kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قول معروف ومغفرة خير من صدقة يتبعها أذى والله غني حليم, باللغة نيانجا

﴿قول معروف ومغفرة خير من صدقة يتبعها أذى والله غني حليم﴾ [البَقَرَة: 263]

Khaled Ibrahim Betala
“Mawu abwino, ndi kukhululukira (amene wakulakwira) nzabwino zedi kuposa sadaka yotsatizidwa ndi masautso. Ndipo Allah ndiyemwe ali Wolemera kwambiri ndiponso Woleza (kwa zolengedwa Zake)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek